Yobu 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtambo umafika kumapeto ake n’kutha.Chimodzimodzi ndi munthu amene wapita ku Manda,* sadzabwerako.+ Salimo 115:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akufa satamanda Ya,+Ngakhalenso aliyense wotsikira kuli chete.+ Yesaya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.
9 Mtambo umafika kumapeto ake n’kutha.Chimodzimodzi ndi munthu amene wapita ku Manda,* sadzabwerako.+
11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.