Yesaya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinanena kuti: “Sindidzamuona Ya,* Ya sindidzamuonanso mʼdziko la amoyo.+ Anthu sindidzawaonansoNdikadzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.
11 Ndinanena kuti: “Sindidzamuona Ya,* Ya sindidzamuonanso mʼdziko la amoyo.+ Anthu sindidzawaonansoNdikadzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.