Yesaya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.
11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.