1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+