Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+

      Musalole kuti ndichite manyazi.

      Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+

  • Salimo 69:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Onse amene akuyembekezera inu asachite manyazi chifukwa cha ine,+

      Inu Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa makamu.+

      Onse amene akufunafuna inu, asanyazitsidwe chifukwa cha ine,+

      Inu Mulungu wa Isiraeli.+

  • Yesaya 50:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ N’chifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Pa chifukwa chimenechi ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi, ndipo ndikudziwa kuti sindidzachita manyazi.+

  • Mateyu 27:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Cha m’ma 3 kolokomo Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena