Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Machitidwe 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+
17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+