Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 77:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+ Salimo 136:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yamikani Wochita zodabwitsa ndiponso ntchito zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+
4 Yamikani Wochita zodabwitsa ndiponso ntchito zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+