1 Mbiri 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anatamanda+ Yehova pamaso pa mpingo wonse,+ kuti: “Mudalitsike+ inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale. Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+ Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+
10 Kenako Davide anatamanda+ Yehova pamaso pa mpingo wonse,+ kuti: “Mudalitsike+ inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale.
68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+