Genesis 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.” Salimo 68:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+
28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”
35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+