Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mulungu anamuuza kuti: “Iwe dzina lako ndi Yakobo.+ Koma kuyambira tsopano, dzina lako silikhalanso Yakobo, ukhala Isiraeli.” Choncho anayamba kumutchula kuti Isiraeli.+

  • 2 Mafumu 17:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Mpaka lero akutsatirabe zipembedzo zawo zakale.+ Palibe amene ankaopa Yehova+ ndipo palibe amene ankatsatira malamulo ake, zigamulo zake,+ ndi chilamulo+ chimene Yehova analamula ana a Yakobo.+ Yakoboyo Mulungu anamusintha dzina n’kumutcha Isiraeli,+

  • Salimo 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+

      Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+

      Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+

  • Salimo 78:71
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+

      Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+

      Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena