Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+

      Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+

  • Salimo 50:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+

      Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,

      Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+

  • Luka 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno abusa aja anabwerera, akulemekeza ndi kutamanda Mulungu chifukwa cha zonse zimene anamva ndi kuziona, ndendende mmene anawauzira muja.

  • 1 Akorinto 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+

  • Chivumbulutso 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena