Salimo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+ Salimo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+
23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+
8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+