Salimo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+ Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+