Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60. Genesis 27:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno Esau anati: “Aka tsopano n’kachiwiri akundichenjerera amene uja!+ Kodi si chifukwa chake dzina lake ndi Yakobo?* Ukulu wanga anatenga kale,+ apa tsopano watenganso madalitso anga!”+ Iye anapitiriza kuti: “Kodi bambo, zoona palibiretu dalitso lililonse limene mwandisungirako?”
26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.
36 Ndiyeno Esau anati: “Aka tsopano n’kachiwiri akundichenjerera amene uja!+ Kodi si chifukwa chake dzina lake ndi Yakobo?* Ukulu wanga anatenga kale,+ apa tsopano watenganso madalitso anga!”+ Iye anapitiriza kuti: “Kodi bambo, zoona palibiretu dalitso lililonse limene mwandisungirako?”