Genesis 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+ Mateyu 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+ Aheberi 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+
34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+
33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+
16 Pakuti anthu polumbira amatchula winawake wamkulu kwa iwo,+ ndipo lumbiro lawo limathetsa mkangano uliwonse, chifukwa kwa iwo lumbiro ndi chotsimikizira chalamulo.+