Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60. Genesis 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.” Hoseya 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene Yakobo anali m’mimba anagwira m’bale wake chidendene.+ Iye analimbana ndi Mulungu ndi mphamvu zake zonse.+
26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.
28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”
3 Pamene Yakobo anali m’mimba anagwira m’bale wake chidendene.+ Iye analimbana ndi Mulungu ndi mphamvu zake zonse.+