Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”

  • Genesis 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mulungu anamuuza kuti: “Iwe dzina lako ndi Yakobo.+ Koma kuyambira tsopano, dzina lako silikhalanso Yakobo, ukhala Isiraeli.” Choncho anayamba kumutchula kuti Isiraeli.+

  • Yesaya 48:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Mverani izi inu a m’nyumba ya Yakobo, inu amene mumadzitcha ndi dzina la Isiraeli,+ amene munatuluka kuchokera m’madzi a Yuda,+ amene mumalumbira pa dzina la Yehova,+ ndiponso inu amene mumaitana Mulungu wa Isiraeli,+ koma osati m’choonadi kapena m’chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena