2 Samueli 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+
21 Poyankha, Davide anauza Mikala kuti: “Ine ndinali kusangalala pamaso pa Yehova amene anandisankha kuti ndikhale mtsogoleri+ wa anthu a Yehova, Aisiraeli, m’malo mwa bambo ako ndi banja lawo lonse, ndipo ndidzasangalala pamaso pa Yehova.+