Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri+ wa anthu ake chifukwa iwe sunasunge zimene Yehova anakulamula.”+

  • 1 Samueli 15:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+

  • 1 Samueli 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patapita nthawi, Yehova anauza Samueli kuti: “Kodi ulirira Sauli+ mpaka liti, pamene ine ndamukana kuti alamulire monga mfumu ya Isiraeli?+ Thira mafuta m’nyanga yako+ ndipo unyamuke. Ndikutumiza kwa Jese+ wa ku Betelehemu, chifukwa ndapeza munthu pakati pa ana ake aamuna woti akhale mfumu yanga.”+

  • 1 Samueli 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+

  • Machitidwe 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena