Rute 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo akazi okhala naye pafupi+ anatcha mwanayo dzina lakuti Obedi.+ Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi ndiye bambo ake a Jese,+ bambo ake a Davide. 1 Mbiri 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Boazi anabereka Obedi,+ Obedi anabereka Jese,+ Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+
17 Pamenepo akazi okhala naye pafupi+ anatcha mwanayo dzina lakuti Obedi.+ Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi ndiye bambo ake a Jese,+ bambo ake a Davide.
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+