Ekisodo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+ 1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+ Salimo 133:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+
25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+
39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+
2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu,+Amene akutsikira kundevu,Ndevu za Aroni,+Amenenso akuyenderera mpaka m’khosi la zovala zake.+