1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+ 1 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.
10 Ndiyeno Samueli anatenga+ botolo ladothi la mafuta ndi kutsanulira mafutawo pamutu wa Sauli, n’kumupsompsona+ ndi kunena kuti: “Yehova wakudzoza iwe kukhala mtsogoleri+ wa cholowa chake.+
22 Pa tsiku limenelo, iwo anadya ndi kumwa mosangalala kwambiri pamaso pa Yehova.+ Kachiwirinso, analonga Solomo mwana wa Davide kukhala mfumu,+ ndi kum’dzoza pamaso pa Yehova kukhala mtsogoleri.+ Anadzozanso Zadoki+ kukhala wansembe.