1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga botolo ladothi lomwe munali mafuta nʼkuthira mafutawo pamutu pa Sauli.+ Kenako anamukisa nʼkunena kuti: “Yehova wakudzoza kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu ake.*+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Tsanzirani, tsa. 73 Nsanja ya Olonda,1/1/2011, tsa. 27
10 Ndiyeno Samueli anatenga botolo ladothi lomwe munali mafuta nʼkuthira mafutawo pamutu pa Sauli.+ Kenako anamukisa nʼkunena kuti: “Yehova wakudzoza kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu ake.*+