1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+ 2 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”
13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+
3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”