Ekisodo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+ 1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+
25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+
13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+