2 Samueli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide pamodzi ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kusangalala pamaso pa Yehova, akuimba mitundu yonse ya zoimbira za mtengo wofanana ndi mtengo wa mkungudza. Anali kuimbanso zeze,+ zoimbira za zingwe,+ zinganga+ ndi maseche+ osiyanasiyana. 2 Samueli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa n’kuti Davide atavala efodi+ wansalu.
5 Davide pamodzi ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kusangalala pamaso pa Yehova, akuimba mitundu yonse ya zoimbira za mtengo wofanana ndi mtengo wa mkungudza. Anali kuimbanso zeze,+ zoimbira za zingwe,+ zinganga+ ndi maseche+ osiyanasiyana.
14 Davide ankavina mozungulira pamaso pa Yehova ndi mphamvu zake zonse. Apa n’kuti Davide atavala efodi+ wansalu.