1 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+ Salimo 150:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mutamandeni ndi chinganga cha mawu osangalatsa.+Mutamandeni ndi chinganga cha mawu amphamvu.+
8 Ndipo Davide ndi Aisiraeli onse anali kusangalala kwadzaoneni+ pamaso pa Mulungu woona. Anali kuimba nyimbo+ ndi azeze,+ zoimbira za zingwe,+ maseche,+ zinganga ndi malipenga.+