1 Mbiri 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalinso oimba awa: Hemani,+ Asafu,+ ndi Etani, kuti aimbe zinganga zamkuwa mokweza.+ 1 Mbiri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Panalinso Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu, ndi Yeyeli.+ Onsewa anali ndi zoimbira za zingwe ndi azeze,+ ndipo Asafu+ anali kuimba zinganga mokweza.+
5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Panalinso Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu, ndi Yeyeli.+ Onsewa anali ndi zoimbira za zingwe ndi azeze,+ ndipo Asafu+ anali kuimba zinganga mokweza.+