18 Iwowa anawaika pamalo awo pamodzi ndi abale awo a gulu lachiwiri.+ Abale awowo anali Zekariya,+ Beni, Yaazieli, Semiramoti, Yehiela, Uni, Eliyabu, Benaya, Maaseya, Matitiya, Elifelehu, Mikineya, ndiponso Obedi-edomu+ ndi Yeyeli, alonda a pachipata.