1 Mbiri 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Matitiya,+ Elifelehu, Mikineya, Obedi-edomu, Yeyeli, ndi Azaziya, anali ndi azeze+ ochunidwa kuti aziimba Seminiti,*+ kuti akhale otsogolera nyimbo. 1 Mbiri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Panalinso Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu, ndi Yeyeli.+ Onsewa anali ndi zoimbira za zingwe ndi azeze,+ ndipo Asafu+ anali kuimba zinganga mokweza.+
21 Matitiya,+ Elifelehu, Mikineya, Obedi-edomu, Yeyeli, ndi Azaziya, anali ndi azeze+ ochunidwa kuti aziimba Seminiti,*+ kuti akhale otsogolera nyimbo.
5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Panalinso Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu, ndi Yeyeli.+ Onsewa anali ndi zoimbira za zingwe ndi azeze,+ ndipo Asafu+ anali kuimba zinganga mokweza.+