1 Mbiri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zotsatira za maerewo zinali motere: Maere oyamba anagwera Yosefe+ mwana wa Asafu, achiwiri anagwera Gedaliya+ (iye ndi abale ake ndi ana ake analipo 12),
9 Zotsatira za maerewo zinali motere: Maere oyamba anagwera Yosefe+ mwana wa Asafu, achiwiri anagwera Gedaliya+ (iye ndi abale ake ndi ana ake analipo 12),