1 Mbiri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu.
2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu.