1 Mbiri 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya,+ Zeri,+ Yesaiya,+ Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya,+ ana 6. Iwowa anali kuyang’aniridwa ndi Yedutuni bambo wawo, amene anali kulosera ndi zeze poyamika ndi potamanda Yehova.+
3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya,+ Zeri,+ Yesaiya,+ Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya,+ ana 6. Iwowa anali kuyang’aniridwa ndi Yedutuni bambo wawo, amene anali kulosera ndi zeze poyamika ndi potamanda Yehova.+