1 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mbuye wathu, chonde, lamulani kuti atumiki anu amene ali pamaso panu akufunireni katswiri+ woimba zeze.+ Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukabwera pa inu, iye azikuimbirani zezeyo, ndipo inu muzipeza bwino.”
16 Mbuye wathu, chonde, lamulani kuti atumiki anu amene ali pamaso panu akufunireni katswiri+ woimba zeze.+ Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukabwera pa inu, iye azikuimbirani zezeyo, ndipo inu muzipeza bwino.”