Genesis 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’bale wake wa Yabala anali Yubala. Ameneyu ndiye anali tate wa onse oimba zeze+ ndi chitoliro.+ Salimo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Yehova poimba zeze.+Muimbireni nyimbo zomutamanda ndi choimbira cha zingwe 10.+