Yobu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo amafuula nthawi zonse poimba maseche ndi azeze.+Amakhala akusangalala poimba zitoliro. Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+