Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 92:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndipo ndidzatero pogwiritsa ntchito choimbira cha zingwe 10 ndi choimbira cha zingwe zitatu.+

      Ndidzaimba nyimbo yomveka bwino ndi zeze.+

  • Salimo 144:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Inu Mulungu, ine ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano.+

      Ndidzaimba nyimbo yokutamandani ndi choimbira cha zingwe 10.+

  • Yesaya 38:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu Yehova bwerani mudzandipulumutse,+ ndipo tidzaimba nyimbo zimene ine ndinapeka. Ndidzaimba ndi zoimbira za zingwe+

      Kunyumba ya Yehova masiku onse a moyo wathu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena