Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti aike m’malo awo abale awo oimba+ okhala ndi zipangizo zoimbira.+ Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe,+ azeze,+ ndi zinganga.+ Anawauza kuti aimbe mokweza kuti nyimbo zachisangalalo zimveke.

  • 2 Mbiri 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa nthawi imeneyi, Hezekiya anaika Alevi+ panyumba ya Yehova atanyamula zinganga,+ zoimbira za zingwe,+ ndi azeze.+ Iwo anali kutsatira ndondomeko yoimbira imene anaikhazikitsa Davide,+ Gadi+ yemwe anali wamasomphenya wa mfumu, ndi mneneri Natani,+ popeza ndondomekoyo inachokera kwa Yehova kudzera mwa aneneri ake.+

  • Salimo 81:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+

      Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena