Salimo 92:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ndidzatero pogwiritsa ntchito choimbira cha zingwe 10 ndi choimbira cha zingwe zitatu.+Ndidzaimba nyimbo yomveka bwino ndi zeze.+ Aefeso 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,
3 Ndipo ndidzatero pogwiritsa ntchito choimbira cha zingwe 10 ndi choimbira cha zingwe zitatu.+Ndidzaimba nyimbo yomveka bwino ndi zeze.+
19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,