Yakobo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pali aliyense mwa inu amene akumva zowawa? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali wina amene akukondwa? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+
13 Kodi pali aliyense mwa inu amene akumva zowawa? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali wina amene akukondwa? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+