Yakobo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pali aliyense amene akukumana ndi mavuto pakati panu? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali aliyense amene akusangalala? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 22-235/15/1993, tsa. 15
13 Kodi pali aliyense amene akukumana ndi mavuto pakati panu? Apitirize kupemphera.+ Kodi pali aliyense amene akusangalala? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.+