Salimo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+ Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+
4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+