Salimo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho moyo wanga ukukondwera, ndipo ndidzakhala wosangalala.+Komanso ndidzakhala wotetezeka.+ Salimo 57:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mtima wanga, galamuka.+Iwe choimbira cha zingwe, galamuka, ndi iwenso zeze.+Ndidzadzuka m’bandakucha usanafike.
8 Iwe mtima wanga, galamuka.+Iwe choimbira cha zingwe, galamuka, ndi iwenso zeze.+Ndidzadzuka m’bandakucha usanafike.