Salimo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho moyo wanga ukukondwera, ndipo ndidzakhala wosangalala.+Komanso ndidzakhala wotetezeka.+ Salimo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+
12 Kuti mtima wanga uimbe nyimbo zokutamandani ndipo usakhale chete.+Inu Yehova Mulungu wanga, ndidzakutamandani mpaka kalekale.+