Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.+Ndidzalengeza ntchito zanu zonse zodabwitsa.+