Salimo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Yehova poimba zeze.+Muimbireni nyimbo zomutamanda ndi choimbira cha zingwe 10.+ 1 Akorinto 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chabwino, zinthu zopanda moyo zimamveka kulira kwake,+ kaya chikhale chitoliro kapena zeze. Koma ngati maliridwe ake angokhala amodzi osasinthasintha, kodi n’zotheka kudziwa nyimbo imene ikuimbidwa ndi chitoliro kapena zezeyo?
7 Chabwino, zinthu zopanda moyo zimamveka kulira kwake,+ kaya chikhale chitoliro kapena zeze. Koma ngati maliridwe ake angokhala amodzi osasinthasintha, kodi n’zotheka kudziwa nyimbo imene ikuimbidwa ndi chitoliro kapena zezeyo?