Genesis 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu. Genesis 46:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Mulungu analankhula ndi Isiraeli m’masomphenya usiku,+ kuti: “Yakobo, Yakobo!” Ndipo Yakobo anayankha kuti: “Ine pano!”+
14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.
2 Ndiyeno Mulungu analankhula ndi Isiraeli m’masomphenya usiku,+ kuti: “Yakobo, Yakobo!” Ndipo Yakobo anayankha kuti: “Ine pano!”+