Numeri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+ Yobu 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+
6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+
15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+