Danieli 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinalota maloto amene anayamba kundichititsa mantha.+ Ndili pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya m’maganizo mwanga. Zimenezi zinayamba kundichititsa mantha.+
5 Kenako ndinalota maloto amene anayamba kundichititsa mantha.+ Ndili pabedi langa ndinaona zithunzithunzi ndi masomphenya m’maganizo mwanga. Zimenezi zinayamba kundichititsa mantha.+