Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Genesis 46:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Mulungu analankhula ndi Isiraeli m’masomphenya usiku,+ kuti: “Yakobo, Yakobo!” Ndipo Yakobo anayankha kuti: “Ine pano!”+ Ekisodo 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu sanawononge atsogoleri amenewo a ana a Isiraeli,+ koma iwo anaona masomphenya a Mulungu woona+ ndipo anadya ndi kumwa.+ Yobu 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+
15 Ndiyeno zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu m’masomphenya,+ kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+
2 Ndiyeno Mulungu analankhula ndi Isiraeli m’masomphenya usiku,+ kuti: “Yakobo, Yakobo!” Ndipo Yakobo anayankha kuti: “Ine pano!”+
11 Mulungu sanawononge atsogoleri amenewo a ana a Isiraeli,+ koma iwo anaona masomphenya a Mulungu woona+ ndipo anadya ndi kumwa.+
15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+